Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 22:15 - Buku Lopatulika

15 Koma Balaki anaonjeza kutumanso akalonga, ochuluka, ndi omveka koposa awa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

15 Koma Balaki anaonjeza kutumanso akalonga, ochuluka, ndi omveka koposa awa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

15 Balaki adatumanso akalonga ochuluka ndi olemekezeka kopambana oyamba aja.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

15 Kenaka Balaki anatumanso akuluakulu ena ambiri ndi olemekezeka kwambiri kuposa oyamba aja ndipo

Onani mutuwo Koperani




Numeri 22:15
4 Mawu Ofanana  

Pamenepo akalonga a Mowabu ananyamuka, nafika kwa Balaki, nati Alikukana Balamu kudza nafe.


Ndipo anadza kwa Balamu, nati kwa iye, Atero Balaki mwana wa Zipori, Pasakhaletu chinthu chakukuletsa kudza kwa ine;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa