Numeri 22:14 - Buku Lopatulika14 Pamenepo akalonga a Mowabu ananyamuka, nafika kwa Balaki, nati Alikukana Balamu kudza nafe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Pamenepo akalonga a Mowabu ananyamuka, nafika kwa Balaki, nati Alikukana Balamu kudza nafe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Tsono akalonga a Mowabu aja adanyamuka napita kwa Balaki, ndipo adakamuuza kuti, “Balamu wakana kubwera.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Kotero akuluakulu a Mowabu anabwerera kwa Balaki ndi kukanena kuti, “Balaamu wakana kubwera nafe.” Onani mutuwo |