Numeri 22:13 - Buku Lopatulika13 Ndipo Balamu anauka m'mawa, nati kwa akalonga a Balaki, Mukani ku dziko lanu; popeza Yehova andikaniza kuti ndisapite nanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndipo Balamu anauka m'mawa, nati kwa akalonga a Balaki, Mukani ku dziko lanu; popeza Yehova andikaniza kuti ndisapite nanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Tsono Balamu adadzuka m'maŵa, naŵauza akalonga a Balaki aja kuti, “Bwererani ku dziko lakwanu, pakuti Chauta sadandilole kuti ndipite nanu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Mmawa mwake Balaamu anadzuka ndi kuwuza akuluakulu a Balaki aja kuti, “Bwererani ku dziko la kwanu chifukwa Yehova sanandilole kuti ndipite nanu.” Onani mutuwo |