Numeri 22:12 - Buku Lopatulika12 Koma Mulungu anati kwa Balamu, Usapita nao; usatemberera anthuwa; pakuti adalitsika. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Koma Mulungu anati kwa Balamu, Usapita nao; usatemberera anthuwa; pakuti adalitsika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Apo Mulungu adauza Balamu kuti, “Usapite nao, ndipo usaŵatemberere anthuwo, chifukwa ngodalitsidwa.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Koma Mulungu anawuza Balaamu kuti, “Usapite nawo. Usawatemberere anthu amenewo chifukwa ndi odalitsika.” Onani mutuwo |