Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 22:16 - Buku Lopatulika

16 Ndipo anadza kwa Balamu, nati kwa iye, Atero Balaki mwana wa Zipori, Pasakhaletu chinthu chakukuletsa kudza kwa ine;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 Ndipo anadza kwa Balamu, nati kwa iye, Atero Balaki mwana wa Zipori, Pasakhaletu chinthu chakukuletsa kudza kwa ine;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 Iwo adafika kwa Balamu namuuza kuti, “Balaki mwana wa Zipora akunena kuti, ‘Musalole kuti chinthu chilichonse chikuletseni kubwera kwa ine.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 anafika kwa Balaamu nati; “Zomwe Balaki mwana wa Zipori akunena ndi izi: ‘Usalole kuti china chilichonse chikulepheretse kubwera kwa ine,

Onani mutuwo Koperani




Numeri 22:16
5 Mawu Ofanana  

Ndipo Abisalomu analamulira anyamata ake, nati, Inu mukhale maso, mtima wa Aminoni ukasekera ndi vinyo, ndipo ine ndikati kwa inu, Kanthani Aminoni; pamenepo mumuphe, musaope; sindine ndakulamulirani inu mulimbike, chitani chamuna.


Pamenepo mfumu inasandutsa Daniele wamkulu, nimpatsa mphatso zazikulu zambiri, namlamuliritsa dera lonse la ku Babiloni; nakhala iye kazembe wamkulu wa anzeru onse a ku Babiloni.


Koma Balaki anaonjeza kutumanso akalonga, ochuluka, ndi omveka koposa awa.


popeza ndidzakuchitira ulemu waukulu, ndipo zonse unena ndi ine ndidzachita; chifukwa chake idzatu, unditembererere anthu awa.


Ndipo Balaki anati kwa Balamu, Kodi sindinatumize kwa iwe ndithu kukakuitana? Unalekeranji kudza kwa ine? Sindikhoza kodi kukuchitira ulemu?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa