Numeri 22:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo Balamu anati kwa Mulungu, Balaki mwana wa Zipori mfumu ya Mowabu, anatumiza kwa ine, ndi kuti, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo Balamu anati kwa Mulungu, Balaki mwana wa Zipori mfumu ya Mowabu, anatumiza kwa ine, ndi kuti, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Balamu adayankha kuti, “Balaki mwana wa Zipora mfumu ya Mowabu, watumiza uthenga kudzandiwuza kuti, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Balaamu anayankha Mulungu kuti, “Balaki mwana wa Zipori, mfumu ya Mowabu, ananditumizira uthenga uwu: Onani mutuwo |