Numeri 22:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo Mulungu anadza kwa Balamu, nati, Anthu awa ali ndi iwe ndiwo ayani? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo Mulungu anadza kwa Balamu, nati, Anthu awa ali ndi iwe ndiwo ayani? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Ndipo Mulungu adadza kwa Balamu namufunsa kuti, “Kodi anthu ali ndi iweŵa ndani?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Mulungu anabwera kwa Balaamu namufunsa kuti, “Kodi anthu ali ndi iwewa ndani?” Onani mutuwo |