Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 22:10 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 Balaamu anayankha Mulungu kuti, “Balaki mwana wa Zipori, mfumu ya Mowabu, ananditumizira uthenga uwu:

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

10 Ndipo Balamu anati kwa Mulungu, Balaki mwana wa Zipori mfumu ya Mowabu, anatumiza kwa ine, ndi kuti,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 Ndipo Balamu anati kwa Mulungu, Balaki mwana wa Zipori mfumu ya Mowabu, anatumiza kwa ine, ndi kuti,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 Balamu adayankha kuti, “Balaki mwana wa Zipora mfumu ya Mowabu, watumiza uthenga kudzandiwuza kuti,

Onani mutuwo Koperani




Numeri 22:10
3 Mawu Ofanana  

‘Taonani, anthu amene achokera ku dziko la Igupto adzaza dziko lonse. Tsopano bwera udzawatemberere mʼmalo mwanga. Mwina ndidzatha kumenyana nawo ndi kuwatulutsa.’ ”


Mulungu anabwera kwa Balaamu namufunsa kuti, “Kodi anthu ali ndi iwewa ndani?”


Mwa anthu ophedwawo munali Evi, Rekemu, Zuri, Huri ndi Reba, mafumu asanu a Amidiyani. Ndipo anaphanso ndi lupanga Balaamu mwana wa Beori.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa