Numeri 21:6 - Buku Lopatulika6 Pamenepo Yehova anatumiza njoka zamoto pakati pa anthu, ndipo zinaluma anthu; nafapo anthu ambiri a Israele. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Pamenepo Yehova anatumiza njoka zamoto pakati pa anthu, ndipo zinaluma anthu; nafapo anthu ambiri a Israele. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Tsono Chauta adatumiza njoka za ululu wonga moto pakati pa anthu aja, ndipo zidaŵaluma, kotero kuti Aisraele ambiri adafa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Choncho Yehova anatumiza njoka zaululu pakati pawo. Zinaluma anthu ndipo Aisraeli ambiri anafa. Onani mutuwo |