Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 21:31 - Buku Lopatulika

31 Chomwecho Israele anakhala m'dziko la Aamori.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

31 Chomwecho Israele anakhala m'dziko la Aamori.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

31 Motero Aisraele adakhala m'dziko la Aamori.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

31 “Choncho Aisraeli anakhala mʼdziko la Aamori.”

Onani mutuwo Koperani




Numeri 21:31
8 Mawu Ofanana  

ndi Aamori, ndi Akanani, ndi Agirigasi, ndi Ayebusi.


Tinawagwetsa; Hesiboni waonongeka kufikira ku Diboni, ndipo tinawapululutsa kufikira ku Nofa. Ndiwo wakufikira ku Medeba.


Ndipo Mose anatumiza anthu akazonde Yazere, nalanda midzi yake, napirikitsa Aamori a komweko.


Ndipo ndinatuma mavu atsogolere inu, amene anawaingitsa pamaso panu, ndiwo mafumu awiri a Aamori; osati ndi lupanga lako, kapena ndi uta wako ai.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa