Numeri 21:32 - Buku Lopatulika32 Ndipo Mose anatumiza anthu akazonde Yazere, nalanda midzi yake, napirikitsa Aamori a komweko. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201432 Ndipo Mose anatumiza anthu akazonde Yazere, nalanda milaga yake, napirikitsa Aamori a komweko. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa32 Mose adatuma anthu kuti akazonde Yazere. Ndipo Aisraele adagwira midzi yake, napirikitsa Aamori amene anali kumeneko. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero32 Mose atatumiza azondi ku Yazeri, Aisraeliwo analanda midzi yozungulira ndi kuthamangitsa Aamori omwe ankakhala kumeneko. Onani mutuwo |