Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 21:30 - Buku Lopatulika

30 Tinawagwetsa; Hesiboni waonongeka kufikira ku Diboni, ndipo tinawapululutsa kufikira ku Nofa. Ndiwo wakufikira ku Medeba.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

30 Tinawagwetsa; Hesiboni waonongeka kufikira ku Diboni, ndipo tinawapululutsa kufikira ku Nofa. Ndiwo wakufikira ku Medeba.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

30 Choncho zidzukulu zao zidatha nkufa, kuyambira ku Hesiboni mpaka ku Diboni, ndipo tidaŵaononga mpaka ku Nofa, pafupi ndi Medeba.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

30 “Koma ife tawagonjetsa; Hesiboni wawonongedwa mʼnjira monse mpaka kufika ku Diboni. Tawaphwasula mpaka ku mzinda wa Nofa, mzinda womwe umafika ku Medeba.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 21:30
13 Mawu Ofanana  

Eni uta anavutitsa iye kwambiri, namponyera iye, namzunza.


Ndipo akuponyawo amene anali palinga anaponya anyamata anu; ndipo anyamata ena a mfumu anafa, ndi mnyamata wanu Uriya Muhiti, iyenso anafa.


Momwemo anadzilembera magaleta zikwi makumi atatu mphambu ziwiri, ndi mfumu ya Maaka ndi anthu ake; nadza iwo, namanga misasa chakuno cha Medeba. Ana a Amoni omwe anasonkhana m'mizinda mwao, nadza kunkhondo.


Ndipo anatuma mivi yake nawabalalitsa; inde mphezi zaunyinji, nawamwaza.


Akwera ku Kachisi, ndi ku Diboni, kumisanje, kukalira; pa Nebo ndi pa Medeba a Mowabu pali kulira; pamitu pao ponse pali dazi, ndevu zonse zametedwa.


Pakuti madzi a Diboni adzala mwazi; pakuti ndidzatengera zina pa Diboni, mkango pa iye amene anapulumuka ku Mowabu, ndi pa otsala a m'dziko.


Iwe mwana wamkazi wokhala mu Diboni, utsike pa ulemerero wako, nukhale ndi ludzu; pakuti wakufunkha Mowabu wakukwerera, iwe waononga malinga ako.


ndi pa Diboni, ndi pa Nebo, ndi pa Betedibilataimu;


Chomwecho Israele anakhala m'dziko la Aamori.


Ataroti, ndi Diboni, ndi Yazere, ndi Nimira, ndi Hesiboni, ndi Eleyale, ndi Sibima, ndi Nebo, ndi Beoni,


Ndipo ana a Gadi anamanga Diboni, ndi Ataroti, ndi Aroere;


Hesiboni ndi mizinda yake yonse yokhala pachidikha; Diboni, ndi Bamoti-Baala ndi Bete-Baala-Meoni;


kuyambira pa Aroere, wokhala m'mphepete mwa chigwa cha Arinoni, ndi mzinda uli pakati pa chigwa, ndi chidikha chonse cha Medeba mpaka ku Diboni;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa