Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 21:19 - Buku Lopatulika

19 atachoka ku Matana ku Nahaliyele; atachoka ku Nahaliyele ku Bamoti;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

19 atachoka ku Matana ku Nahaliyele; atachoka ku Nahaliyele ku Bamoti;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

19 kuchokera ku Matana adafika ku Nahaliyele, kuchokera ku Nahaliyele adafika ku Bamoti.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

19 Kuchoka ku Matana anapita ku Nahalieli, kuchoka ku Nahalieli anapita ku Bamoti,

Onani mutuwo Koperani




Numeri 21:19
3 Mawu Ofanana  

chitsime adakumba mafumu, adachikonza omveka a anthu; atanena mlamuli, ndi ndodo zao. Ndipo atachoka kuchipululu anamuka ku Matana;


atachoka ku Bamoti ku chigwa chili m'dziko la Mowabu, ku mutu wa Pisiga, popenyana ndi chipululu.


Hesiboni ndi mizinda yake yonse yokhala pachidikha; Diboni, ndi Bamoti-Baala ndi Bete-Baala-Meoni;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa