Numeri 21:20 - Buku Lopatulika20 atachoka ku Bamoti ku chigwa chili m'dziko la Mowabu, ku mutu wa Pisiga, popenyana ndi chipululu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 atachoka ku Bamoti ku chigwa chili m'dziko la Mowabu, ku mutu wa Pisiga, popenyana ndi chipululu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Kuchokera ku Bamoti adafika ku chigwa cha m'dziko la Mowabu, kudzera njira ya pamwamba pa phiri la Pisiga, loyang'anana ndi chipululu cham'munsi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 ndipo atachoka ku Bamoti anapita ku chigwa cha dziko la Mowabu kudzera njira ya pamwamba pa phiri la Pisiga, moyangʼanana ndi Yesimoni. Onani mutuwo |