Numeri 21:18 - Buku Lopatulika18 chitsime adakumba mafumu, adachikonza omveka a anthu; atanena mlamuli, ndi ndodo zao. Ndipo atachoka kuchipululu anamuka ku Matana; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 chitsime adakumba mafumu, adachikonza omveka a anthu; atanena mlamuli, ndi ndodo zao. Ndipo atachoka kuchipululu anamuka ku Matana; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Chitsime chimene adakumba mafumu, chimene atsogoleri omveka a anthu adakumba, adakumba ndi ndodo zao zaufumu ndiponso ndi ndodo zao zoyendera.” Kuchokera kuchipululu, Aisraele adafika ku Matana, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 chitsime chomwe anakumba mafumu, chomwe anakumba anthu omveka, ndi ndodo zawo zaufumu ndi ndodo zawo zoyendera.” Kenaka anachoka ku chipululu ndi kupita ku Matana. Onani mutuwo |