Numeri 21:17 - Buku Lopatulika17 Pamenepo Israele anaimba nyimbo iyi, Tumphuka chitsime iwe; muchithirire mang'ombe; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Pamenepo Israele anaimba nyimbo iyi, Tumphuka chitsime iwe; muchithirire mang'ombe; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Tsono Aisraele adaimba nyimbo iyi yakuti, “Tulutsa madzi ako, chitsime iwe, ife tiŵaimbira nyimbo! Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Pamenepo Aisraeli anayimba nyimbo iyi: “Tulutsa madzi, chitsime iwe! Chiyimbireni nyimbo, Onani mutuwo |