Numeri 21:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo atachokapo anamuka ku Beere, ndicho chitsime chimene Yehova anachinena kwa Mose, Sonkhanitsa anthu, ndipo ndidzawapatsa madzi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo atachokapo anamuka ku Beere, ndicho chitsime chimene Yehova anachinena kwa Mose, Sonkhanitsa anthu, ndipo ndidzawapatsa madzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Kuchokera kumeneko adapitirira mpaka ku malo oti Beeri. Chimenecho chinali chitsime chimene Chauta adaalozera Mose namuuza kuti, “Uŵasonkhanitse pamodzi anthuwo, ndipo ndidzaŵapatsa madzi.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Kuchokera kumeneko anapitirira mpaka ku Beeri, pa chitsime chomwe Yehova anawuza Mose kuti, “Sonkhanitsa anthu pamodzi ndipo ndidzawapatsa madzi.” Onani mutuwo |