Numeri 20:26 - Buku Lopatulika26 nuvule Aroni zovala zake, numveke Eleazara mwana wake; ndipo Aroni adzaitanidwa kunka kwa anthu a mtundu wake, nadzafa komweko. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 nuvule Aroni zovala zake, numveke Eleazara mwana wake; ndipo Aroni adzaitanidwa kunka kwa anthu a mtundu wake, nadzafa komweko. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Kumeneko umvule Aroni zovala zaunsembe ndi kuveka mwana wake Eleazara. Ndipo Aroni adzafera komweko.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Uvule Aaroni zovala zake ndipo umuveke mwana wake Eliezara, pakuti Aaroni adzafera komweko, ndipo adzakakhala ndi anthu a mtundu wake.” Onani mutuwo |