Numeri 20:27 - Buku Lopatulika27 Pamenepo Mose anachita monga adamulamula Yehova; ndipo anakwera m'phiri la Hori pamaso pa khamu lonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 Pamenepo Mose anachita monga adamulamula Yehova; ndipo anakwera m'phiri la Hori pamaso pa khamu lonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 Mose adachitadi zimene Chauta adamlamula. Atatu onsewo adakwera phiri la Horo, mpingo wonse ukupenya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 Mose anachita monga Yehova anamulamulira: Anapita ku phiri la Hori gulu lonse likuona. Onani mutuwo |