Numeri 20:25 - Buku Lopatulika25 Tenga Aroni ndi Eleazara mwana wake, nukwere nao m'phiri la Hori; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Tenga Aroni ndi Eleazara mwana wake, nukwere nao m'phiri la Hori; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Utenge Aroni pamodzi ndi Eleazara mwana wake, ukwere nawo pamwamba pa phiri la Horo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Tenga Aaroni ndi mwana wake wamwamuna Eliezara ndipo ukwere nawo ku phiri la Hori. Onani mutuwo |