Numeri 20:22 - Buku Lopatulika22 Ndipo anayenda ulendo kuchokera ku Kadesi; ndi ana a Israele, ndilo khamu lonse, anadza kuphiri la Hori. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Ndipo anayenda ulendo kuchokera ku Kadesi; ndi ana a Israele, ndilo khamu lonse, anadza kuphiri la Hori. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Tsono mpingo wonse wa Aisraele udanyamuka ku Kadesi kuja nukafika ku phiri la Horo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Gulu lonse la Aisraeli linachoka ku Kadesi ndipo linafika ku phiri la Hori. Onani mutuwo |