Numeri 20:21 - Buku Lopatulika21 Potero Edomu anakana kulola Israele kupitira pa malire ake; chifukwa chake Aisraele anampatukira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Potero Edomu anakana kulola Israele kupitira pa malire ake; chifukwa chake Aisraele anampatukira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Motero Edomu sadavomere kuti Aisraele adutse m'dziko mwake. Ndipo Aisraele adadzera njira ina. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Edomu anakaniza Israeli kuti adutse mʼdziko lake, choncho Israeli anabwerera. Onani mutuwo |