Numeri 20:20 - Buku Lopatulika20 Koma anati, Usapitirepo. Ndipo Edomu anatulukira kukumana naye ndi anthu ambiri, ndi dzanja lamphamvu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Koma anati, Usapitirepo. Ndipo Edomu anatulukira kukumana naye ndi anthu ambiri, ndi dzanja lamphamvu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Koma Edomu adaŵayankha kuti, “Simudutsa ai.” Pamenepo Edomu adatuluka ndi gulu lankhondo lalikulu ndi lamphamvu kukalimbana ndi Aisraele. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Koma Edomu anayankhanso kuti, “Musadutse.” Kenaka Edomu anatuluka ndi gulu lankhondo lalikulu komanso lamphamvu. Onani mutuwo |