Numeri 20:23 - Buku Lopatulika23 Ndipo Yehova ananena ndi Mose ndi Aroni m'phiri la Hori, pa malire a dziko la Edomu, ndi kuti, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Ndipo Yehova ananena ndi Mose ndi Aroni m'phiri la Hori, pa malire a dziko la Edomu, ndi kuti, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Ku phiri limenelo, limene lili m'malire a dziko la Edomu, Chauta adauza Mose ndi Aroni kuti, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Ali pa phiri la Hori, pafupi ndi malire a Edomu, Yehova anati kwa Mose ndi Aaroni, Onani mutuwo |