Numeri 20:15 - Buku Lopatulika15 kuti makolo athu anatsikira kunka ku Ejipito, ndipo tinakhala mu Ejipito masiku ambiri; ndipo Aejipito anachitira zoipa ife, ndi makolo athu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 kuti makolo athu anatsikira kunka ku Ejipito, ndipo tinakhala m'Ejipito masiku ambiri; ndipo Aejipito anachitira zoipa ife, ndi makolo athu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Pajatu makolo athu adaapita ku Ejipito, ndipo tidakhala kumeneko zaka zambiri. Aejipito adatizunza ife ndi makolo athu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Makolo athu anapita ku Igupto ndipo tinakhala kumeneko zaka zambiri. Aigupto anatizunza pamodzi ndi makolo athuwo, Onani mutuwo |