Numeri 20:14 - Buku Lopatulika14 Pamenepo Mose anatumiza amithenga ochokera ku Kadesi kumuka kwa mfumu ya Edomu, ndi kuti, Atero mbale wanu Israele, Mudziwa zowawa zonse zinatigwera; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Pamenepo Mose anatumiza amithenga ochokera ku Kadesi kumuka kwa mfumu ya Edomu, ndi kuti, Atero mbale wanu Israele, Mudziwa zowawa zonse zinatigwera; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Ali ku Kadesi, Mose adatuma amithenga kwa mfumu ya ku Edomu kuti akanene kuti, “Abale anu Aisraele akuti, ‘Mukudziŵa mavuto onse amene atigwera, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Mose anatumiza amithenga kuchokera ku Kadesi kupita kwa mfumu ya ku Edomu, kukanena kuti, “Mʼbale wako Israeli akunena izi: Inuyo mukudziwa za mavuto onse amene anatigwera. Onani mutuwo |