Numeri 2:30 - Buku Lopatulika30 Ndi khamu lake, ndi owerengedwa ake, ndiwo zikwi makumi asanu mphambu zitatu kudza mazana anai. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 Ndi khamu lake, ndi owerengedwa ake, ndiwo zikwi makumi asanu mphambu zitatu kudza mazana anai. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 ndipo ankhondo ake ngokwanira 53,400. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 53,400. Onani mutuwo |