Numeri 18:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo musunge udikiro wa malo opatulika, ndi udikiro wa guwa la nsembe; kuti pasakhalenso mkwiyo pa ana a Israele. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo musunge udikiro wa malo opatulika, ndi udikiro wa guwa la nsembe; kuti pasakhalenso mkwiyo pa ana a Israele. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Mudzatumikira pa ntchito za m'malo opatulika ndi pa ntchito za guwa, kuti mkwiyo usaŵagwerenso Aisraele. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 “Inuyo muzisamalira malo wopatulika ndi guwa lansembe, kuti ukali wa Yehova usawagwerenso Aisraeli. Onani mutuwo |