Numeri 18:4 - Buku Lopatulika4 Koma aziphatikana nawe, nazisunga udikiro wa chihema chokomanako, kuchita ntchito yonse ya chihema; koma mlendo asayandikize inu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Koma aziphatikana nawe, nazisunga udikiro wa chihema chokomanako, kuchita ntchito yonse ya chihema; koma mlendo asayandikize inu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Iwo adzagwira nawe ntchito, ndi kumatumikiranso m'chihema chamsonkhano pa ntchito zonse zam'chihemamo. Ndipo wina aliyense asadzafike pafupi ndi inu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Azikhala ndi inu ndipo azisamalira ntchito yonse ya mu tenti ya msonkhano koma munthu wina aliyense wapadera sayenera kufika pafupi nanu. Onani mutuwo |