Numeri 16:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo Mose ananena ndi Kora, Tamvani tsono, inu ana a Levi; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo Mose ananena ndi Kora, Tamvani tsono, inu ana a Levi; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Mose adauza Kora kuti, “Imvani tsono inu Alevi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Mose anawuzanso Kora kuti, “Inu Alevi, tsopano tamverani! Onani mutuwo |