Numeri 16:49 - Buku Lopatulika49 Koma akufa nao mliri ndiwo zikwi khumi ndi zinai mphambu mazana asanu ndi awiri, osawerenga aja adafera chija cha Kora. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201449 Koma akufa nao mliri ndiwo zikwi khumi ndi zinai mphambu mazana asanu ndi awiri, osawerenga aja adafera chija cha Kora. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa49 Komabe amene adafa ndi mliriwo anali 14,700, kuwonjeza pa anthu aja amene adafa pa mlandu wa Kora. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero49 Komabe anthu 14, 700 anafa ndi mliriwo, kuwonjezera pa aja amene anafa chifukwa cha Kora. Onani mutuwo |