Numeri 16:50 - Buku Lopatulika50 Ndipo Aroni anabwera kwa Mose ku khomo la chihema chokomanako; ndi mliri unaleka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201450 Ndipo Aroni anabwera kwa Mose ku khomo la chihema chokomanako; ndi mliri unaleka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa50 Pambuyo pake Aroni adabwerera kwa Mose ku chipata cha chihema chamsonkhano, mliriwo utaleka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero50 Ndipo Aaroni anabwerera kwa Mose ku khomo la tenti ya msonkhano, chifukwa mliriwo unali utatha. Onani mutuwo |