Numeri 16:48 - Buku Lopatulika48 Ndipo anaima pakati pa akufa ndi amoyo; ndi mliri unaleka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201448 Ndipo anaima pakati pa akufa ndi amoyo; ndi mliri unaleka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa48 Aroni adakaima pakati pa anthu akufa ndi amoyo aja, ndipo mliriwo udaleka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero48 Iye anayimirira pakati pa anthu amoyo ndi akufa ndipo mliri unaleka. Onani mutuwo |