Numeri 15:34 - Buku Lopatulika34 Ndipo anayamba wamsunga, popeza sichinanenedwe choyenera kumchitira iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Ndipo anathanga wamsunga, popeza sichinanenedwa choyenera kumchitira iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 Iwo adamponya m'ndende chifukwa choti sankadziŵa bwino zoti amchite. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 ndipo anamutsekera mʼndende chifukwa sankadziwa choti achite naye. Onani mutuwo |