Numeri 15:35 - Buku Lopatulika35 Ndipo Yehova anati kwa Mose, Amuphe munthuyu ndithu; khamu lonse limponye miyala kunja kwa chigono. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201435 Ndipo Yehova anati kwa Mose, Amuphe munthuyu ndithu; khamu lonse limponye miyala kunja kwa chigono. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa35 Tsono Chauta adauza Mose kuti, “Munthuyo aphedwe. Mpingo wonse umponye miyala kunja kwa mahema.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero35 Pamenepo Yehova anawuza Mose kuti, “Munthu ameneyu ayenera kuphedwa. Gulu lonse liyenera kumugenda ndi miyala kunja kwa msasa.” Onani mutuwo |