Numeri 15:33 - Buku Lopatulika33 Ndipo amene adampezawo alinkufuna nkhuni anabwera naye kwa Mose ndi Aroni, ndi kwa khamu lonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201433 Ndipo amene adampezawo alinkufuna nkhuni anabwera naye kwa Mose ndi Aroni, ndi kwa khamu lonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa33 Amene adapeza munthuyo akutola nkhuni, adabwera naye kwa Mose ndi Aroni ndi kwa mpingo wonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero33 Amene anamupeza akutola nkhunizo anabwera naye kwa Mose ndi Aaroni ndi kwa gulu lonse Onani mutuwo |