Numeri 15:32 - Buku Lopatulika32 Ndipo pokhala ana a Israele m'chipululu, anapeza munthu wakufuna nkhuni tsiku la Sabata. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201432 Ndipo pokhala ana a Israele m'chipululu, anapeza munthu wakufuna nkhuni tsiku la Sabata. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa32 Pamene Aisraele anali m'chipululu muja, adapeza munthu akutola nkhuni pa tsiku la Sabata. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero32 Aisraeli ali mʼchipululu, munthu wina anapezeka akutola nkhuni tsiku la Sabata. Onani mutuwo |