Numeri 15:31 - Buku Lopatulika31 Popeza ananyoza mau a Yehova, nathyola lamulo lake; munthuyu amsadze konse; mphulupulu yake ikhale pa iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 Popeza ananyoza mau a Yehova, nathyola lamulo lake; munthuyu amsadze konse; mphulupulu yake ikhale pa iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 Popeza kuti wanyoza mau a Chauta ndipo waphwanya lamulo la Chauta, amchotseretu munthu ameneyo, tchimo lake lidzamkangamira.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 Popeza wanyoza mawu a Yehova ndi kuphwanya malamulo ake. Munthu ameneyo achotsedwe ndithu, kuchimwa kwake kudzakhala pa iyeyo.’ ” Onani mutuwo |