Numeri 15:27 - Buku Lopatulika27 Ndipo akachimwa munthu mmodzi osati dala, abwere nayo mbuzi yaikazi ya chaka chimodzi, ikhale nsembe yauchimo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 Ndipo akachimwa munthu mmodzi osati dala, abwere nayo mbuzi yamsoti ya chaka chimodzi, ikhale nsembe yauchimo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 “Ngati munthu mmodzi alakwa mosadziŵa, apereke mbuzi yaikazi ya chaka chimodzi kuti ikhale nsembe yopepesera machimo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 “ ‘Koma ngati munthu mmodzi achimwa mosadziwa, ayenera kubweretsa mbuzi yayikazi ya chaka chimodzi kuti ikhale nsembe yopepesera machimo. Onani mutuwo |