Numeri 15:26 - Buku Lopatulika26 Ndipo khamu lonse la ana a Israele, adzakhululukidwa, ndi mlendo yemwe wakukhala pakati pao; popeza khamu lonse linachichita osati dala. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Ndipo khamu lonse la ana a Israele, adzakhululukidwa, ndi mlendo yemwe wakukhala pakati pao; popeza khamu lonse linachichita osati dala. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 mpingo wonse wa Aisraele udzakhululukidwa pamodzi ndi mlendo yemwe amene akhala pakati pao, poti anthu onse adalakwa mosadziŵa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Gulu lonse la Aisraeli ndi alendo okhala pakati pawo adzakhululukidwa chifukwa anthu onsewo anachimwa mosadziwa. Onani mutuwo |