Numeri 15:23 - Buku Lopatulika23 ndizo zonse Yehova anakuuzani ndi dzanja la Mose, kuyambira tsikulo Yehova analamula, ndi kunkabe m'mibadwo yanu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 ndizo zonse Yehova anakuuzani ndi dzanja la Mose, kuyambira tsikulo Yehova anauza, ndi kunkabe m'mibadwo yanu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 ndi zonse zimene adakulamulani kudzera mwa Mose, kuyambira tsiku limene Chauta adapereka lamulo mpaka m'tsogolo mwake pa mibadwo yanu yonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 lina lililonse mwa malamulo a Yehova amene wapereka kwa inu kudzera mwa Mose, kuyambira tsiku limene Yehova anawapereka mpaka mibado ya mʼtsogolo, Onani mutuwo |