Numeri 15:22 - Buku Lopatulika22 Ndipo pamene mulakwa, osachita mau awa onse amene Yehova ananena ndi Mose; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Ndipo pamene mulakwa, osachita mau awa onse amene Yehova ananena ndi Mose; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 “Koma mwina mutha kulakwa mosadziŵa, osasunga malamulo onse amene Chauta adauza Mose, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 “ ‘Ndipo ngati muchimwa mosadziwa posasunga ena mwa malamulo awa amene Yehova wapereka kwa Mose, Onani mutuwo |