Numeri 15:18 - Buku Lopatulika18 Nena ndi ana a Israele, nuti nao, Pamene mulowa m'dziko limene ndilikukulowetsani, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Nena ndi ana a Israele, nuti nao, Pamene mulowa m'dziko limene ndilikukulowetsani, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 “Uza Aisraele kuti, ‘Mukadzaloŵa m'dziko m'mene ndidzakufikitsani, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 “Yankhula ndi Aisraeli ndipo unene kuti, ‘Mukakalowa mʼdziko limene ndikukutengeraniko Onani mutuwo |