Numeri 15:19 - Buku Lopatulika19 kudzali, pakudya inu mkate wa m'dzikolo, muzikwezera Yehova nsembe yokweza. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 kudzali, pakudya inu mkate wa m'dzikolo, muzikwezera Yehova nsembe yokweza. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 ndipo mukamadzadya buledi wam'dzikolo, mudzapereke nsembe kwa Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 ndipo mukakadya chakudya cha mʼdzikolo, mukapereke gawo lina kwa Yehova monga chopereka. Onani mutuwo |