Numeri 15:16 - Buku Lopatulika16 Pakhale chilamulo chimodzi ndi chiweruzo chimodzi kwa inu ndi kwa mlendo wakukhala kwanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Pakhale chilamulo chimodzi ndi chiweruzo chimodzi kwa inu ndi kwa mlendo wakukhala kwanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Kwa inu ndi kwa mlendo wokhala pakati panu, pakhale lamulo limodzi ndi mwambo umodzi wokha.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Mudzakhale ndi malamulo ndi miyambo yofanana, inuyo ndi mlendo wokhala pakati panu.’ ” Onani mutuwo |
Ndipo Aisraele onse, ndi akulu ao, ndi akapitao ao, ndi oweruza ao anaima chakuno ndi chauko cha likasa, pamaso pa ansembe Alevi, akusenza likasa la chipangano la Yehova, mbadwa ndi alendo omwe; ena a iwo pandunji paphiri la Gerizimu, ndi ena pandunji paphiri la Ebala; monga Mose, mtumiki wa Yehova, adalamulira poyamba paja kuti adalitse anthu a Israele.