Numeri 15:12 - Buku Lopatulika12 Monga mwa kuwerenga kwake kwa izi muzikonza, muzitero ndi yonse monga mwa kuwerenga kwake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Monga mwa kuwerenga kwake kwa izi muzikonza, muzitero ndi yonse monga mwa kuwerenga kwake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Zingachuluke chotani nyama zoperekedwazo, muchite choncho ndi nyama iliyonse, mpaka zonse kutha. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Ngakhale zingachuluke chotani, chitani izi kwa iliyonse ya nyamazo. Onani mutuwo |