Numeri 15:13 - Buku Lopatulika13 Onse akubadwa m'dzikomo achite izi momwemo, pobwera nayo kwa Yehova nsembe yamoto ya fungo lokoma. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Onse akubadwa m'dzikomo achite izi momwemo, pobwera nayo kwa Yehova nsembe yamoto ya fungo lokoma. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Mbadwa zonse zizichita motero pamene zikupereka nsembe yotentha pa moto, yotulutsa fungo lokomera Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 “ ‘Mbadwa iliyonse ya mu Israeli izichita zimenezi pamene ibweretsa nsembe yotentha pa moto kuti ikhale fungo lokoma kwa Yehova. Onani mutuwo |