Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 15:11 - Buku Lopatulika

11 Kudzatero ndi ng'ombe iliyonse, kapena nkhosa yamphongo iliyonse, kapena mwanawankhosa aliyense, kapena mwanawambuzi aliyense.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Kudzatero ndi ng'ombe iliyonse, kapena nkhosa yamphongo iliyonse, kapena mwanawankhosa aliyense, kapena mwanawambuzi aliyense.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 “Umu ndimo m'mene zidzachitikire ndi ng'ombe yamphongo iliyonse, kapena nkhosa yamphongo, kapena mwanawankhosa aliyense kapena mwanawambuzi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Ngʼombe yayimuna iliyonse kapena nkhosa yayimuna iliyonse, mwana wankhosa aliyense kapena mbuzi yayingʼono, zizikonzedwa motere.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 15:11
5 Mawu Ofanana  

Mulankhule ndi gulu lonse la Israele ndi kuti, Tsiku lakhumi la mwezi uno adzitengere munthu yense mwanawankhosa, monga mwa mabanja a atate ao, mwanawankhosa pabanja.


Ndipo ubwere naye vinyo wa nsembe yothira limodzi la magawo awiri la hini, ndiye nsembe yamoto ya fungo lokoma, ya Yehova.


Monga mwa kuwerenga kwake kwa izi muzikonza, muzitero ndi yonse monga mwa kuwerenga kwake.


ndipo uzikonzera nsembe yopsereza kapena yophera, vinyo wa nsembe yothira, limodzi la magawo anai la hini, ukhale wa mwanawankhosa mmodzi.


pamodzi ndi nsembe yopsereza ya pamwezi, ndi nsembe yake yaufa, ndi nsembe yopsereza yosalekeza, ndi nsembe yake yaufa, ndi nsembe zake zothira, monga mwa lemba lake, zikhale za fungo lokoma, nsembe yamoto ya Yehova.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa