Numeri 14:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo Yoswa mwana wa Nuni, ndi Kalebe mwana wa Yefune, ndiwo a iwo aja adazonda dzikolo, anang'amba zovala zao; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo Yoswa mwana wa Nuni, ndi Kalebe mwana wa Yefune, ndiwo a iwo aja adazonda dzikolo, anang'amba zovala zao; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Yoswa mwana wa Nuni, ndi Kalebe mwana wa Yefune, amene adaali m'gulu la anthu okazonda dziko lija, adang'amba zovala zao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Yoswa mwana wa Nuni ndi Kalebe mwana wa Yefune, omwe anali amodzi mwa amene anakazonda nawo dziko, anangʼamba zovala zawo Onani mutuwo |