Numeri 14:42 - Buku Lopatulika42 Musakwereko, pakuti Yehova sali pakati pa inu; kuti angakukantheni adani anu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201442 Musakwereko, pakuti Yehova sali pakati pa inu; kuti angakukantheni adani anu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa42 Musapite, kuti mungaphedwe pamaso pa adani anu, pakuti Chauta sali nanu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero42 Musapite chifukwa Yehova sali pakati panu. Mudzagonjetsedwa ndi adani anu Onani mutuwo |